Job 39:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ungadalire njatiyo chifukwa cha mphamvu zake? Kodi ungayembekeze kuti ikugwirira ntchito yako?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Udzaikhulupirira kodi, popeza mphamvu yake njaikulu? Udzaisiyira ntchito yako kodi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ungadalire njatiyo chifukwa champhamvu zake? Kodi ungayilekere kuti igwire ntchito zako zolemetsa?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Udzaikhulupirira kodi, popeza mphamvu yace njaikuru? Udzaisiyira nchito yako kodi?