Job 39:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Nthiŵatiŵa ikukupiza mapiko ake monyadira, koma nthenga zake ndi mapiko ake sizikuithandiza kuuluka monga amachitira kakoŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Phiko la nthiwatiwa likondwera, koma mapiko ndi nthenga zake nzofatsa kodi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Nthiwatiwa imakupiza mapiko ake monyadira, koma mapikowo sangafanane ndi mapiko ndi nthenga za kakowa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Phiko la nthiwatiwa likondwera, Koma mapiko ndi nthenga zace nzofatsa kodi?