Job 39:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma imaiŵala kuti mapazi ake omwe angathe kuphwanya mazirawo, ndipo kuti nyama zakuthengo nkuŵapondereza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
niiwala kuti phazi lingawaphwanye, kapena chilombo chingawapondereze.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
nthiwatiwayo sidera nkhawa kuti mazira ake angathe kuswanyidwa, ndi kuti nyama zakuthengo zitha kuwaponda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Niiwala kuti phazi lingawaphwanye, Kapena cirombo cingawapondereze.