Job 39:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthiŵatiŵa imachita ana ake nkhalwe ngati si ake. Zakuti idaavutika poŵabereka imaiŵalako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iumira mtima ana ake monga ngati sali ake; idzilemetsa ndi ntchito chabe, popeza ilibe mantha;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthiwatiwa imachitira nkhanza ana ake ngati anawo si ake; Imayiwala zoti inavutika powabala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iumira mtima ana ace monga ngati sali ace; Idzilemetsa ndi nchito cabe, popeza iribe mantha;