Job 39:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe nthiŵatiŵayo ikadzambatuka nkuyamba kuthaŵa, imamsiya kutali kavalo ndi wokwerapo wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ikafika nthawi yake, iweramuka, iseka kavalo ndi wa pamsana pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komatu nthiwatiwa ikadzambatuka ndi kuyamba kuthamanga, imamusiya kutali kavalo ndi wokwerapo wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ikafika nthawi yace, iweramuka, Iseka kavalo ndi wa pamsana pace.