Job 39:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akavalowo amanjenjemera ndi ukali nathamangira kutsogolo, ndipo akangomva lipenga sangathe kuima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi kunjenjemera kwaukali aimeza nthaka, osaimitsika pomveka lipenga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kavaloyo amanjenjemera ndi ukali ndi kulumphalumpha; satha kungoyima pamene wamva kulira kwa lipenga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi kunjenjemera kwaukali aimeza nthaka, Osaimitsika pomveka lipenga.