Job 39:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Lipenga likalira amati, ‘Twee!’ Amamva fungo la nkhondo ali patali. Amamva kufuula kwa atsogoleri ankhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pomveka lipenga akuti, Hee! Anunkhiza nkhondo ilikudza kutali, kugunda kwa akazembe ndi kuhahaza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Lipenga likalira amati, ‘Twee!’ Amamva fungo la nkhondo ali patali, kufuwula kwa anthu olamulira nkhondo ndi mfuwu wankhondo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pomveka lipenga akuti, Hee! Anunkhiza nkhondo irikudza kutali Kugunda kwa akazembe ndi kuhahaza,