Job 39:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi umalamula chiwombankhanga ndiwe kuti chiziwuluka? Kodi udachiphunzitsa ndiwe kukamanga chisa pamwamba penipeni?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi chiombankhanga chikwera m'mwamba pochilamulira iwe, nichimanga chisanja chake m'mwamba?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi umalamulira chiwombankhanga ndiwe kuti chiziwuluka ndi kumanga chisa chake pamwamba penipeni?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi ciombankhanga cikwera m'mwamba pocilamulira iwe, Nicimanga cisanja cace m'mwamba?