Job 39:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine ndidaŵapatsa chipululu kuti chikhale malo ao okhalako, ndiponso chichere kuti chikhale dera lao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
imene ndachiyesa chipululu nyumba yake, ndi dziko lakhulo pokhala pake?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndinamupatsa chipululu kuti chikhale mudzi wake, nthaka ya mchere kuti ikhale malo ake okhalamo
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Imene ndaciyesa cipululu nyumba yace, Ndi dziko lakhulo pokhala pace?