Job 39:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amakhala kutali ndi mizinda yaphokoso, ndipo sadziŵa mau okuwa a anthu oyendetsa nyama zakatundu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Aseka phokoso la kumudzi, osamva kukuwa kwa wofulumiza nyama za m'goli.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amakhala kutali ndi phokoso la mu mzinda; ndipo samva kufuwula kwa oyendetsa nyama zakatundu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Aseka phokoso la kumudzi, Osamva kukuwa kwa wofulumiza nyama za m'goli.