Job 4:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu oipa amakhuluma ngati mkango, koma Mulungu amaŵathyola mano.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kubangula kwa mkango, ndi kulira kwa mkango waukali kwaletsedwa, ndi mano a misona ya mkango athyoledwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mikango imabangula ndi kulira, komabe mano a mikango yamphamvu amathyoledwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kubangula kwa mkango, ndi kulira kwa mkango waukali kwaletsedwa, Ndi mano a misona ya mkango atyoledwa.