Job 4:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwowo amafa ngati mikango yosoŵa nyama, ndipo misona yao imamwazikana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mkango wokalamba udzifera posowa mkoka, ndi misona ya mkango waukazi imwazika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mkango umafa chifukwa chosowa nyama, ndipo ana amkango amamwazikana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mkango wokalamba udzifera posowa mkoka, Ndi misona ya mkango waukazi imwazika.