Job 4:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Tsono mau adandifika monong'ona, khutu langa lidamva kunong'onako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anditengera mau m'tseri, m'khutu mwanga ndinalandira kunong'oneza kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mawu anabwera kwa ine mwamseri, makutu anga anamva kunongʼona kwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anditengera mau m'tseri, M'khutu mwanga ndinalandira kunong'oneza kwace.