Job 4:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo mpweya wayaziyazi udandidutsa kumaso, ndipo ubweya wa pathupi panga udangoti njoo, kuimirira, chifukwa cha mantha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo panapita mzimu pamaso panga; tsitsi la thupi langa lidati nyaunyau.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo mzimu unadutsa pamaso panga, ndipo ubweya wa pa thupi langa unayima kuti njoo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo panapita mzimu pamaso panga; Tsitsi la thupi langa lidati nyau nyau.