Job 4:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe Yobe, kodi wina atakuyankha, ndiye kuti wakulakwira? Ah, koma ine ndekha sindingathe kukhala chete.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu akayesa kunena nawe mau, kodi udzamva nao chisoni? Koma akhoza ndani kudziletsa kunena?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngati wina atakuyankha, kodi ungakhumudwe? Koma ndani angakhale chete wosayankhula?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu akayesa kunena nawe mau, kodi udzamva nao cisoni? Koma akhoza ndani kudziletsa kunena?