Job 4:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'maŵa ali moyo, madzulo nkufa munthuyo. Amapita ku manda, naiŵalika kotheratu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuyambira m'mawa kufikira madzulo athudzuka; aonongeka kosatha, osasamalirako munthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mmawa ali moyo, pofika madzulo afa; mwakachetechete, amawonongeka kwamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuyambira m'mawa kufikira madzulo athudzuka; Aonongeka kosatha, osasamalirako munthu.