Job 4:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Taona, iwe waphunzitsa anthu ambiri, walimbitsa mtima anthu ofooka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taona iwe walangiza aunyinji, walimbitsa manja a ofooka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Taganiza momwe iwe walangizira anthu ambiri, momwe walimbitsira anthu ofowoka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taona iwe walangiza aunyinji, Walimbitsa manja a ofoka.