Job 4:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Unkalemekeza Mulungu, tsono uyenera kumdalira Iyeyo, Unkayenda m'njira yosalakwa, tsono uyenera kukhulupirira Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi kulimbika mtima kwako si ndiko kuti uopa Mulungu, ndi chiyembekezo chako si ndiwo ungwiro wa njira zako?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi kuopa Mulungu kwako sindiko kulimbika mtima kwako? Ndipo moyo wako wosalakwa ndiye chiyembekezo chako?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi kulimbika mtima kwako si ndiko kuti uopa Mulungu, Ndi ciyembekezo cako si ndiwo ungwiro wa njira zako?