Job 4:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ganiza bwino tsopano: Kodi alipo munthu wosachimwa amene adaonongekapo nkale lonse? Nanga nkuti kumene udaona anthu olungama ataphedwa?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Takumbukira tsopano, watayika ndani wosapalamula konse? Kapena oongoka mtima alikhidwa kuti?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ganiza bwino tsopano: Kodi munthu wosalakwa anawonongekapo nʼkale lonse? Nʼkuti kumene munthu wolungama mtima anaphedwa?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Takumbukila tsopano, watayika ndani wosaparamula konse? Kapena oongoka mtima alikhidwa kuti?