Job 4:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga ndaonera ine, anthu amene amabzala tchimo namafesa mavuto, amakolola zomwezo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga umo, ndaonera, olimira mphulupulu, nabzala vuto, akololapo zomwezo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga ndaonera ine, anthu amene amatipula zoyipa, ndi iwo amene amadzala mavuto, amakolola zomwezo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga umo ndaonera, olimira mphulupulu, Nabzala bvuto, akololapo zomwezo.