Job 4:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga momwe mphepo ya mkuntho imasakazira zinthu, Mulungu amaŵaononga ndi mkwiyo wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atayika ndi mpweya wa Mulungu, nathedwa ndi mpumo wa mkwiyo wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amaphedwa ndi mpweya wa Mulungu; amawonongeka ndi mpweya waukali wa mkwiyo wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atayika ndi mpweya wa Mulungu, Nathedwa ndi mpumo wa mkwiyo wace.