Job 40:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Taganiza za mvuu, Ine ndidaipanga monga momwe ndidapangira iwe. Imadya udzu ngati ng'ombe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tapenya tsono mvuu ndinaipanga pamodzi ndi iwe, ikudya udzu ngati ng'ombe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Taganiza za mvuwu, imene ndinayipanga monga momwe ndinapangira iwe, ndipo imadya udzu ngati ngʼombe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tapenya tsono mvuu ndinaipanga pamodzi ndi iwe, Ikudya udzu ngati ng'ombe.