Job 40:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mphamvu zake ndi zazikulu kwambiri, thupi lake ndi lanyonga zedi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tapenya tsono, mphamvu yake ili m'chuuno mwake, ndi kulimbalimba kwake kuli m'mitsempha ya m'mimba yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mphamvu zake ndi zazikulu kwambiri, thupi lake ndi lanyonga kwambiri!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tapenya tsono, mphamvu yace iri m'cuuno mwace, Ndi kulimbalimba kwace kuli m'mitsempha ya m'mimba yace.