Job 40:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Imaimiritsa mchira wake kuti tototo, ngati mtengo wa mkungudza. Mitsempha ya ntchafu zake ndi yogwirana bwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Igwedeza mchira wake ngati mkungudza; mitsempha ya ntchafu zake ipotana.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mchira wake umayima tolotolo ngati mtengo wamkungudza; mitsempha ya ntchafu zake ndi yogwirana bwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Igwedeza mcira wace ngati mkungudza; Mitsempha ya ncafu zace ipotana.