Job 40:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mvuu ndiyo yaikulu mwa zolengedwa za Ine Mulungu. Ine amene ndidailenga ndidaipatsa maso ake oopsa aja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iyo ndiyo chiyambi cha machitidwe a Mulungu; wakuilenga anaininkha lupanga lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mvuwuyo ndi yayikulu mwa zolengedwa za Mulungu, komatu mlengi wake amatha kuyiopseza ndi lupanga lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iyo ndiyo ciyambi ca macitidwe a Mulungu; Wakuilenga anaininkha lupanga lace.