Job 40:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi nanga alipo wina amene angathe kukola mvuu ndi mbedza kapena kuikola mu msampha?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ikakhala maso, munthu adzaigwira kodi? Kapena kuboola m'mphuno mwake ili m'khwekhwe?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi alipo amene angathe kukola mvuwu ndi mbedza kapena kuyikola mu msampha?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ikakhala maso, munthu adzaigwira kodi? Kapena kuboola m'mphuno mwace iri m'khwekhwe?