Job 40:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ungandiyese ine wolakwa? Kodi ungandidzudzule kuti iweyo ukhale wolungama?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chingakhale chiweruzo changa udzachithyola kodi? Udzanditsutsa kuti ndili woipa kodi, kuti ukhale wolungama ndiwe?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kodi iwe unganyoze chiweruzo changa cholungama? Kodi ungandidzudzule kuti iweyo ukhale wolungama?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cingakhale ciweruzo canga udzacityola kodi? Udzanditsutsa kuti ndiri woipa kodi, kuti ukhale wolungama ndiwe?