Job 41:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ungathe kuchikoka ndi mbedza ya nsomba chilombo chija cha Leviyatani, kapena kukanikiza lilime lake pansi ndi chingwe?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi ukhoza kukoka Leviyatani ndi mbedza? Kapena kukanikiza kalandira wake ndi chingwe?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kodi ungathe kukoka ngʼona ndi mbedza ya nsomba kapena kukanikiza lilime lake pansi ndi chingwe?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi ukhoza kukoka ng'ona ndi mbedza? Kapena kukanikiza kalandira wace ndi cingwe?