Job 41:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndani angasende chikopa chake? Ndani angachibaye chikopa chimene chija, kulimba konse kuja ngati chovala chachitsulo?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndani adzasenda chovala chake chakunja? Adzalowa ndani kumizere iwiri ya mano ake?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndani angasende chikopa chake? Ndani angayiyandikire kuti abowole chikopa chake cholimbacho?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndani adzasenda cobvala cace cakunja? Adzalowa ndani ku mizere iwiri ya mano ace?