Job 41:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuyetsemula kwake kumatulutsa mbaliwali, maso ake amaŵala ngati kuŵala kwa mbandakucha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuyetsemula ing'anipitsa kuunika, ndi maso ake akunga zikope za m'mawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuyetsemula kwake kumatulutsa mbaliwali; maso ake amawala ngati kuwala kwa mʼbandakucha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuyetsemula ing'anipitsa kuunika, Ndi maso ace akunga zikope za m'mawa.