Job 41:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'kamwa mwake mumatuluka nsakali za moto, mumathetheka mbaliwali za moto.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'kamwa mwake mutuluka miuni, mbaliwali za moto zibukamo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼkamwa mwake mumatuluka nsakali zamoto ndipo mumathetheka mbaliwali zamoto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'kamwa mwace muturuka miuni, Mbaliwali za moto zibukamo.