Job 41:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ungathe kuchimanga chingwe m'mphuno mwake, kapena kuchiboola nsagwada ndi mbedza?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi ukhoza kumanga m'mphuno ndi mlulu? Kapena kuboola nsagwada wake ndi mbedza?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ungathe kumanga chingwe mʼmphuno mwake, kapena kubowola nsagwada zake ndi mbedza?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi ukhoza kumanga m'mphuno ndi mlulu? Kapena kuboola nsagwada wace ndi momba?