Job 41:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mpweya wake umayatsa makala, malaŵi a moto amatuluka m'kamwa mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
mpweya wake uyatsa makala, ndi m'kamwa mwake mutuluka lawi la moto.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mpweya wake umayatsa makala, ndipo malawi amoto amatuluka mʼkamwa mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mpweya wace uyatsa makara, Ndi m'kamwa mwace muturuka lawi la moto.