Job 41:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chilombocho chikangoti vuuku, ndi amphamvu omwe amaopa. Akamva phokoso lake, amachita mantha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ikanyamuka, amphamvu achita mantha; chifukwa cha kuopsedwa azimidwa nzeru.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngʼonayo ikangovuwuka, ndi anthu amphamvu omwe amaopa; amabwerera mʼmbuyo, kuthawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ikanyamuka, amphamvu acita mantha; Cifukwa ca kuopsedwa azimidwa nzeru.