Job 41:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Za kumimba kwake zili ngati mapale akuthwa. Chimatambalala m'matope ngati galeta lopunthira tirigu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kumimba kwake ikunga mapale akuthwa, itasalala kuthope ngati chopunthira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mamba a ku mimba kwake ali ngati chopunthira chakunthwa ndipo imasiya mkukuluzi mʼmatope ngati galeta lopunthira tirigu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kumimba kwace ikunga mapale akuthwa, Itasalala kuthope ngati copunthira.