Job 41:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumbuyo kwake chimasiya nthubwitubwi zambee, kotero kuti munthu angaganize kuti nyanja yachita imvi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ichititsa mifunde yonyezimira pambuyo pake; munthu akadati pozama pali ndi imvi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kumbuyo kwake imasiya nthubwitubwi zambee, kotero kuti munthu angaganize kuti nyanja yachita imvi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Icititsa mifunde yonyezimira pambuyo pace; Munthu akadati pozama pali ndi imvi.