Job 41:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ungaseŵere nacho ngati mbalame? Kodi kapena nkuchimanga ndi unyolo kuti adzakazi ako aseŵere nacho?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi udzasewera nayo ngati mbalame? Kapena udzaimangira anamwali ako kuti aiwete?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi udzasewera nayo ngati mbalame, kapena kuyimangirira kuti atsikana ako asewere nayo?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi udzasewera nayo ngati mbalame? Kapena udzaimangira anamwali ako kuti aiwete?