Job 41:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi asodzi nkuchitsatsa malonda? Nanga amalondawo nkugaŵanagaŵana nyama yake kuti akaigulitse?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi opangana malonda adzaitsatsa? Adzaigawana eni malonda?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi anthu adzayitsatsa malonda? Nanga amalondawo nʼkugawanagawana nyama yake kuti akagulitse?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi opangana malonda adzaitsatsa? Adzaigawana eni malonda?