Job 42:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wamkulu mwa ana aakazi aja adamutcha Yemima. Wachiŵiri anali Keziya, wachitatu anali Kerehapuki.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamutcha dzina la woyamba Yemima, ndi dzina la wachiwiri Keziya, ndi dzina la wachitatu Kerenihapuki.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wake wamkazi woyamba anamutcha Yemima, wachiwiri anamutcha Keziya, wachitatu anamutcha Kereni Hapuki.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamucha dzina la woyamba Yemima, ndi dzina la waciwiri Keziya, ndi dzina la wacitatu Kerenihapuki.