Job 42:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'dziko monsemo munalibe akazi okongola ngati ana a Yobe. Bambo wao adaŵapatsa choloŵa chimodzimodzi ngati alongo ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'dziko monse simunapezeka akazi okongola ngati ana akazi a Yobu, nawapatsa cholowa atate wao pamodzi ndi alongo ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼdziko monsemo munalibe akazi okongola ngati ana a Yobu, ndipo abambo awo anawapatsa cholowa pamodzi ndi alongo awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'dziko monse simunapezeka akazi okongola ngati ana akazi a Yobu, nawapatsa colowa atate wao pamodzi ndi alongo ao.