Job 42:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake ndikuchita manyazi ndi zonse zimene ndidakamba, ndikulapa podzithira fumbi ndi phulusa.” Mulungu adalitsanso Yobe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa chake ndekha ndidzinyansa, ndi kulapa m'fumbi ndi mapulusa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake ndi kuchita manyazi, ndikulapa podzithira fumbi ndi phulusa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace ndekha ndidzinyansa, ndi kulapa M'pfumbi ndi mapulusa.