Job 42:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Elifazi wa ku Temani, Bilidadi wa ku Suki ndi Zofari wa ku Naama adapita, nakachita zimene Chauta adaŵauza. Ndipo Chauta adamveradi pemphero la Yobe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Namuka Elifazi wa ku Temani, ndi Bilidadi Msuki, ndi Zofari wa ku Naama, nachita monga Yehova adawauza; ndipo Yehova anavomereza Yobu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Motero Elifazi wa ku Temani, Bilidadi wa ku Suki ndi Zofari wa ku Naama anachita zimene Yehova anawawuza ndipo Yehova anamvera pemphero la Yobu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Namuka Elifazi wa ku Temani, ndi Bilidadi Msuki, ndi Zofara wa ku Naama, nacita monga Yehova adawauza; ndipo Yehova anabvomereza Yobu.