Job 5:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amakola anthu ochenjera mu msampha wa kuchenjera kwao, amathetsa msanga zimene akapsala adakonza kuti achite.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akola eni nzeru m'kuchenjera kwao, ndi uphungu wa opotoka mtima usonthokera pachabe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amakola anthu ochenjera mu msampha wa kuchenjera kwawo, ndipo zolinga za atambwali amazithetsa msangamsanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akola eni nzeru m'kucenjerera kwao, Ndi uphungu wa opotoka mtima usonthokera pacabe,