Job 5:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwowo amakumana ndi mdima ngakhale masana, amayambasa masanasana ngati usiku.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo akomana ndi mdima pali dzuwa, nayambasa dzuwa lili pakati pamtu monga usiku.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mdima umawagwera nthawi yamasana; nthawi yamasana amayenda moyambasayambasa monga nthawi ya usiku.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo akomana ndi mdima pali dzuwa, Nayambasa dzuwa liri pakati pamtu monga usiku.