Job 5:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Mulungu amateteza amphaŵi kwa adani oŵasinjirira, amapulumutsa osauka kwa anthu ofuna kuŵapanikiza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Apulumutsa aumphawi kulupanga la kukamwa kwao, ndi kudzanja la wamphamvu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu amapulumutsa amphawi ku lupanga la mʼkamwa mwawo; amawapulumutsa mʼmanja mwa anthu amphamvu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Apulumutsa aumphawi ku lopanga La kukamwa kwao, ndi ku dzanja la wamphamvu.