Job 5:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ndi wodala munthu amene Mulungu amamdzudzula. Nchifukwa chake usamanyoze chilango cha Mphambe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taona, wodala munthu amene Mulungu amdzudzula; chifukwa chake usapeputsa kulanga kwa Wamphamvuyonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Wodala munthu amene Mulungu amamudzudzula; nʼchifukwa chake usanyoze chilango cha Wamphamvuzonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taona, wodala munthu amene Mulungu amdzudzula; Cifukwa cace usapeputsa kulanga kwa Wamphamvuyonse.