Job 5:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa nthaŵi ya njala adzakusamala, pa nthaŵi ya nkhondo adzakupulumutsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzakuombola kuimfa m'njala, ndi kumphamvu ya lupanga m'nkhondo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nthawi ya njala adzakulanditsa ku imfa, ndipo nthawi ya nkhondo adzakupulumutsa ku lupanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzakuombola kuimfa m'njala, Ndi ku mphamvu ya lupanga m'nkhondo.