Job 5:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzakuteteza kwa anthu osinjirira, chiwonongeko chikadzafika, sudzachiwopa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Udzabisikira mkwapulo wa lilime, sudzachiopanso chikadza chipasuko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adzakuteteza kwa anthu osinjirira, ndipo palibe chifukwa chochitira mantha pamene chiwonongeko chafika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Udzabisikira mkwapulo wa lilime, Sudzaciopanso cikadza cipasuko.