Job 5:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'minda mwako simudzakhala miyala, nyama zakuthengo sizizakuvuta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti udzakhala ndi pangano ndi miyala ya kuthengo; ndi nyama za kuthengo zidzakhala nawe mumtendere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti udzachita pangano ndi miyala ya mʼmunda mwako, ndipo nyama zakuthengo zidzakhala nawe mwamtendere.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti udzakhala ndi pangano ndi miyala ya kuthengo; Ndi nyama za kuthengo zidzakhala nawe mumtendere.