Job 5:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Udzadziŵa kuti ana ako adzakhala ambiri, ndipo kuti zidzukulu zako zidzachuluka ngati udzu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Udzapezanso kuti mbeu zako zidzachuluka, ndi obala iwe ngati zitsamba za padziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Udzadziwa kuti ana ako adzakhala ambiri, ndipo zidzukulu zako zidzakhala ngati udzu wa mʼdziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Udzapezanso kuti mbeu zako zidzacuruka, Ndi obala iwe ngati zitsamba za padziko.